Joel 3:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ku Yudako kudzakhala anthu mpaka muyaya, ndipo ku Yerusalemu sikudzatha anthu pa mibadwo yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yuda adzakhala chikhalire, ndi Yerusalemu ku mibadwomibadwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yuda adzakhala ndi anthu mpaka muyaya ndi Yerusalemu ku mibadomibado.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yuda adzakhala cikhalire, ndi Yerusalemu ku mibadwo mibadwo.