Joel 3:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudatenga siliva ndi golide wanga ndi zinthu zanga zina zamtengowapatali, kupita nazo ku nyumba za milungu yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza inu munatenga siliva wanga ndi golide wanga, ndi kulonga zofunika zanga zokoma m'akachisi anu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti munatenga siliva ndi golide wanga ndi kupita nacho chuma changa chamtengowapatali ku nyumba zanu zopembedzera mafano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza inu munatenga siliva wanga ndi golidi wanga, ndi kulonga zofunika zanga zokoma m'akacisi anu;