Joel 3:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudakagulitsa anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu kwa Agriki, kuti mupite nawo kutali ndi malire a dziko lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
munagulitsanso ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu kwa ana a Yavani, kuwachotsa kutali kwa malire ao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munagulitsa anthu a ku Yuda ndi Yerusalemu kwa Agriki, kuti apite kutali ndi malire a dziko lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
munagulitsanso ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu kwa ana a Yavani, kuwacotsa kutali kwa malire ao;