Joel 3:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndidzaŵadzutsa kuti achoke kumalo kumene mudaŵagulitsa. Kenaka ndidzabwezera zochita zanu zonse pamutu panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
taonani, ndidzawautsa kumalo kumene munawagulitsako, ndi kubwezera chilango chanu pamutu panu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Taonani, Ine ndidzawachotsa kumalo kumene munawagulitsako, ndipo ndidzabwezera zimene mwachita pa mitu yanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
taonani, ndidzawautsa kumalo kumene munawagulitsako, ndi kubwezera cilango canu pamutu panu;
Recommended Reading