John 1:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa Iyeyo munali moyo, ndipo moyowo unali kuŵala kounikira anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa Iye munali moyo; ndi moyowu unali kuunika kwa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa Iye munali moyo, ndipo moyowo unali kuwunika kwa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa iye munali moyo; ndi moyowu unali kuunika kwa anthu.