John 1:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Filipo anali wa ku mudzi wa Betsaida, kwaonso kwa Andrea ndi Petro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Filipo anali wa ku Betsaida, mudzi wa Andrea ndi Petro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Filipo monga Andreya ndi Petro, anali wochokera ku mzinda mudzi Betisaida.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Filipo anali wa ku Betsaida, mudzi wa Andreya ndi Petro.