John 1:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adaatuma munthu wina, dzina lake Yohane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lake ndiye Yohane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunabwera munthu amene anatumizidwa kuchokera kwa Mulungu; Iyeyo dzina lake linali Yohane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lace ndiye Yohane.