John 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuŵala kwenikweni, kounikira anthu onse, kunkadza pansi pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uku ndiko kuunika kwenikweni, kumene kuunikira anthu onse akulowa m'dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwunika koona kumene kuwunikira munthu aliyense kunabwera ku dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uku ndiko kuunika kweni kweni, kumene kuunikira anthu onse akulowa m'dziko lapansi.