John 10:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adaayambanso kutsutsana okhaokha chifukwa cha mau ameneŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Panakhalanso kutsutsana pakati pa Ayuda chifukwa cha mau awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa mawu awa Ayuda anagawikananso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Panakhalanso kutsutsana pakati pa Ayuda cifukwa ca mau awa.