John 10:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambiri mwa iwo ankati, “Ali ndi mizimu yoipa, ndipo wapenga. Bwanji mukumumveranso Iyeyu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ambiri mwa iwo ananena, Ali ndi chiwanda, nachita misala; mukumva Iye bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambiri a iwo anati, “Iye ndi wogwidwa ndi ziwanda ndi wamisala. Chifukwa chiyani mukumvera Iye?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ambiri mwa iwo ananena, Ali ndi ciwanda, nacita misala; mukumva iye bwanji?