John 10:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ku Yerusalemu kunali chikondwerero chokumbukira kuperekedwanso kwa Nyumba ya Mulungu. Inali nyengo yozizira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunali phwando la kukonzetsanso m'Yerusalemu; nyengoyo ndi yachisanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Yerusalemu kunali chikondwerero chokumbukira kupatulidwa kwa Nyumba ya Mulungu. Inali nthawi yozizira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kunali phwando la kukonzersanso m'Yerusalemu; nyengoyo ndi yacisanu.