John 10:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akazitulutsa nkhosa zake zonse, amazitsogolera, izo nkumamtsatira, chifukwa zimadziŵa mau ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene adatulutsa zonse nkhosa zimtsata iye; chifukwa zidziwa mau ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akazitulutsa nkhosa zake zonse, iye amazitsogolera, ndipo nkhosa zakezo zimamutsata chifukwa zimadziwa mawu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene adaturutsa zonse za iye yekha, azitsogolera; ndi nkhosa zimtsata iye; cifukwa zidziwa mau ace.