John 10:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mlendo sizidzamtsatira ai, zidzamthaŵa, chifukwa sizidziŵa mau a alendo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mlendo sizidzamtsata, koma zidzamthawa; chifukwa sizidziwa mau a alendo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nkhosazo sizidzatsatira mlendo. Izo zidzamuthawa chifukwa sizizindikira mawu a mlendo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mlendo sizidzamtsata, koma zidzamthawa; cifukwasizidziwa mau a alendo.