John 11:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akayenda usiku, amakhumudwa chifukwa kuŵalako alibe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati munthu ayenda usiku, akhumudwa, chifukwa mulibe kuunika mwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma amene akuyenda usiku amapunthwa, chifukwa kuwalako alibe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati munthu ayenda usiku, akhumudwa, cifukwa mulibe kuunika mwa iye.