John 11:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo ophunzira ake adati, “Ambuye, ngati wagona tulo, achira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, ngati ali m'tulo adzachira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzira ake anayankha kuti, “Ambuye, ngati wagona adzapeza bwino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace akuphunzira ace anati kwa iye, Ambuye, ngati ali m'tulo adzacira.