John 11:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Marita adati, “Ndikudziŵa kuti adzauka podzauka anthu kwa akufa pa tsiku lomaliza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Marita ananena ndi Iye, Ndidziwa kuti adzauka m'kuuka tsiku lomaliza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Marita anayankha kuti, “Ine ndikudziwa kuti adzauka pa kuukanso pa tsiku lomaliza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Marita ananena ndi iye, Ndidziwa kuti adzauka m'kuuka tsiku lomariza.