John 11:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Marita atanena zimenezi, adaitanira paseri Maria mng'ono wake namuuza kuti, “Afika Aphunzitsi, akukuitana.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene anati ichi anachoka naitana Maria mbale wake m'tseri, ndi kuti, Wafika Mphunzitsi, akuitana iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye atanena izi anabwerera ndi kukayitana mchemwali wake Mariya namuyankhula monongʼona pambali, nati, “Aphunzitsi abwera ndipo akukuyitana.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene anati ici anacoka naitana Mariya mbale wace m'tseri, ndi kuti, Wafika Mphunzitsi, akuitana iwe.