John 11:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maria atamva zimenezi, adanyamuka msangamsanga, nadza kwa Yesu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iyeyo, pakumva, ananyamuka msanga, nadza kwa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mariya atamva izi, anayimirira mofulumira napita kwa Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iyeyo, pakumva, ananyamuka msanga, nadza kwa iye.