John 11:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adaŵafunsa kuti, “Mudamuika kuti?” Iwo adati, “Ambuye, tiyeni mukaone.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Mwamuika iye kuti? Ananena ndi Iye, Ambuye, tiyeni mukaone.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anafunsa kuti, “Kodi mwamuyika kuti?” Iwo anayankha kuti, “Ambuye tiyeni mukaone.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, Mwamuika iye kuti? Ananena ndi iye, Ambuye, tiyeni, mukaone.