John 11:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo anthu aja adati, “Onani, ankamukonda zedi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Ayuda ananena, Taonani, anamkondadi!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Ayuda anati, “Taonani mmene Iye anamukondera Lazaro!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Ayuda ananena, Taonani, anamkondadi!