John 11:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tikamlekerera chomwechi, anthu onse adzamkhulupirira, ndipo Aroma adzabwera nkudzatiwonongera malo athu oyeraŵa ndiponso mtundu wathuwu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati timleka Iye kotero, onse adzakhulupirira Iye; ndipo adzadza Aroma nadzachotsa malo athu ndi mtundu wathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ife timuleka kuti apitirize chotere, aliyense adzamukhulupirira Iye, ndipo kenaka Aroma adzabwera ndi kudzatenga malo athu pamodzi ndi dziko lathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati timleka iye kotero, onse adzakhulupirira iye; ndipo adzadza Aroma nadzacotsa malo athu ndi mtundu wathu.