John 11:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuyambira tsiku limenelo akulu aja a Ayuda adayamba kupangana zoti amuphe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake, kuyambira tsiku lomwelo anapangana kuti amuphe Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho kuyambira tsiku limeneli iwo anakonzekera za kuti amuphe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace, kuyambira tsiku Iomwelo anapangana kuti amuphe iye.