John 11:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe pamene adamva za matendawo, Yesu adaswera masiku aŵiri pamalo pomwe adaaliripo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pa malo pomwepo masiku awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma atamva kuti Lazaro akudwala, Iye anakhalabe kumene anali masiku ena awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pa malo pomwepo masiku awiri.