John 12:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero akulu a ansembe adaapangana zoti aphe ndi Lazaro yemwe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ansembe aakulu anapangana kuti akaphe Lazaronso;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho akulu a ansembe anakonza njira yoti aphenso Lazaro,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ansembe akulu anapangana kuti akaphe Lazaronso;