John 12:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti chifukwa cha iyeyo anthu ambiri ankaŵachokera nkumakhulupirira Yesu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti ambiri a Ayuda anachoka chifukwa cha iye, nakhulupirira Yesu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti chifukwa cha iye Ayuda ambiri amapita kwa Yesu ndi kumukhulupirira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti ambiri a Ayuda anacoka cifukwa ca iye, nakhulupirira Yesu.