John 12:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yesu adapeza mwanawabulu nakwerapo, monga akunenera Malembo kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yesu, m'mene adapeza kabulu anakhala pamenepo; monga mulembedwa:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anapeza bulu wamngʼono ndi kukwerapo, monga kunalembedwa kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yesu, m'mene adapeza kaburu anakhala pamenepo; monga mulembedwa: