John 12:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma panali Agriki ena pakati pa anthu amene adaakapembedza pa chikondwererocho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma panali Agriki ena mwa iwo akukwera kunka kukalambira pachikondwerero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano panali Agriki ena pakati pa amene anapita kukapembedza ku phwando.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma panali Ahelene ena mwa iwo akukwera kunka kukalambira paphwando,