John 12:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zidaatero kuti zipherezere zimene mneneri Yesaya adaaneneratu kuti, “Ambuye, ndani wakhulupirira kulalika kwathu? Ndani wazindikira mphamvu za Ambuye pa zimenezi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mau a Yesaya mneneri akakwaniridwe, amene anati, Ambuye, wakhulupirira ndani kulalikira kwathu? Ndipo mkono wa Ambuye wavumbulutsidwa kwa yani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi zinakwaniritsa mawu a mneneri Yesaya kuti: “Ambuye, wakhulupirira uthenga wathu ndani, ndipo ndi kwa yani komwe mkono wa Ambuye wavumbulutsidwa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mau a Yesaya mneneri akakwaniridwe, amene anati, 3 Ambuye, wakhulupirira ndani kulalikira kwathu? Ndipo mkono wa Ambuye wabvumbulutsidwa kwa yani?