John 12:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo sadathe kukhulupirira, chifukwa paja Yesaya yemweyo adaanenanso kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha ichi sanathe kukhulupirira, pakuti Yesaya anatinso,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chifukwa cha ichi iwo sanakhulupirire, chifukwa Yesaya ananenanso kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca ici sanathe kukhulupira, pakuti Yesaya anatinso,