John 12:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesaya ponena mau amenewo, ankanena za Yesu, chifukwa adaaona ulemerero wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Izi anati Yesaya, chifukwa anaona ulemerero wake; nalankhula za Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesaya ananena izi chifukwa anaona ulemerero wa Yesu ndi kuyankhula za Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
5 Izi anati Yesaya, cifukwa anaona ulemerero wace; nalankhula za iye.