John 12:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe ambiri mwa atsogoleri ao omwe adakhulupirira Yesu. Koma chifukwa cha Afarisi iwo sankanena zimenezo poyera. Ankaopa kuti angaŵadule ku mpingo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kungakhale kotero, ambiri a mwa akulu anakhulupirira Iye; koma chifukwa cha Afarisi sanavomereza, kuti angaletsedwe m'sunagoge,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe pa nthawi yomweyi ambiri ngakhale atsogoleri anakhulupirira Iye. Koma chifukwa cha Afarisi iwo sanavomereze chikhulupiriro chawo chifukwa amaopa kuti angawatulutse mʼsunagoge;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kungakhale kotero, ambiri a mwa akuru anakhulupirira iye; koma 6 cifukwa ca Afarisi sanabvomereza, kuti angaletsedwe m'sunagoge,