John 12:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankakonda kuti azilandira ulemu kwa anthu koposa kulandira ulemu kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti anakonda ulemerero wa anthu koposa ulemerero wa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti iwo amakonda kuyamikiridwa ndi anthu kuposa kuyamikiridwa ndi Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
7 pakuti anakonda ulemerero wa anthu koposa ulemerero wa Mulungu.