John 13:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu ankamudziŵa munthu wodzampereka kwa adani ake, nchifukwa chake adaati, “Si nonsenu muli oyera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anadziwa amene adzampereka Iye; chifukwa cha ichi anati, Simuli oyera nonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Iye anadziwa amene adzamupereka, ndipo nʼchifukwa chake anati saliyense wa inu ali woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anadziwa amene adzampereka iye; cifukwa ca ici anati, Simuli oyera nonse.