John 13:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndakupatsani chitsanzo, kuti inunso muzichita monga momwe Ine ndakuchitirani inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndakupatsani inu chitsanzo, kuti, monga Ine ndakuchitirani inu, inunso muchite.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndakupatsani chitsanzo kuti muzichita monga Ine ndachitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndakupatsani inu citsanzo, kuti, monga Ine ndakucitirani inu, inunso mucite.