John 13:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati mudziŵa zimenezi, ndinu odala mukamazichita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mudziwa izi, odala inu ngati muzichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati inu mudziwa zinthu zimenezi, mudzakhala odala mukamazichita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mudziwa izi, odala inu ngati muzicita.