John 13:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzira aja adayamba kupenyetsetsana, osadziŵa konse kuti akunena yani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ophunzira analikupenyana wina kwa mnzake, ndi kusinkhasinkha kuti ananena za yani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzira ake anapenyetsetsana wina ndi mnzake, posadziwa kuti amanena za yani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akuphunzira analikupenyanawina kwa mnzace, ndi kusinkhasinkha kuti ananena za yani.