John 13:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mwa amene ankadyawo panalibe ndi mmodzi yemwe amene adaamvetsa zimene adaamuuzazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma palibe mmodzi wa iwo akuseamako anadziwa chimene anafuna, poti atere naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma panalibe ndi mmodzi yemwe pa chakudyapo amene anamvetsa chifukwa chimene Yesu ananenera izi kwa iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kama palibe mmodzi wa iwo akuseamako anadziwa cimene anafuna, poti atere naye.