John 13:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukamakondana, anthu onse adzadziŵa kuti ndinudi ophunzira anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa ichi adzazindikira onse kuti muli ophunzira anga, ngati muli nacho chikondano wina ndi mnzake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukamakondana aliyense adzadziwa kuti ndinu ophunzira anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
1 Mwa ici adzazindikira onse kuti muli akuphunzira anga, ngati muli naco cikondano wina ndi mnzace.