John 13:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Petro adamufunsa kuti, “Ambuye, chifukwa chiyani sindingathe kukutsatirani tsopano? Inetu nditha kutaya ngakhale moyo wanga chifukwa cha Inu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Petro ananena ndi Iye, Ambuye, sindingathe kukutsatani Inu tsopano chifukwa ninji? Ndidzataya moyo wanga chifukwa cha Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Petro anafunsa kuti, “Ambuye, nʼchifukwa chiyani ine sindingakutsatireni tsopano? Ine ndidzapereka moyo wanga chifukwa cha Inu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Petro ananena ndi iye, Ambuye, sindingathe kukutsatani Inu tsopano cifukwa ninji? 3 Ndidzataya moyo wanga cifukwa ca Inu.