John 13:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Simoni Petro adati, “Ambuye, ngati ndi choncho, mutsuke osati mapazi anga okha, komanso manja anga ndi mutu womwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Simoni Petro ananena ndi Iye, Ambuye, si mapazi anga okha, komanso manja ndi mutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Simoni Petro anayankha kuti, “Ambuye, osati mapazi okha komanso manja anga ndi mutu wanga womwe!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Simoni Petro ananena ndi iye, Ambuye, si mapazi anga okha, komanse manja ndi mutu.