John 14:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidzakusiyani nokha kuti mukhale ana amasiye. Ndidzabweranso kwa inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindidzakusiyani inu mukhale ana amasiye; ndidza kwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine sindikusiyani nokha kuti mukhale ana amasiye. Ine ndidzabweranso kwa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindidza-kusiyani inu mukhale ana amasiye; ndidza kwa inu.