John 14:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo kumene ndikupita Ineko, njira yake mukuidziŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kumene ndinkako Ine, mudziwa njira yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mukudziwa njira ya kumene Ine ndikupita.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kumene ndinkako Ine, mudziwa njira yace.