John 15:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lamulo langa ndi lakuti muzikondana monga momwe Ine ndakukonderani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lamulo langa ndi ili, kuti mukondane wina ndi mnzake, monga ndakonda inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lamulo langa ndi ili: ‘Kondanani wina ndi mnzake monga Ine ndakonda inu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lamulo langa ndi ili, kuti mukondane wina ndi mnzace, monga ndakonda inu.