John 15:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho lamulo langa ndi lakuti muzikondana.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zinthu izi ndilamula inu, kuti mukondane wina ndi mnzake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lamulo langa ndi ili: ‘Muzikondana.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zinthu izi ndilamulira inu, kuti mukondane wina ndi mnzace.