John 15:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha Ine, popeza kuti samdziŵa amene adandituma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma izi zonse adzakuchitirani chifukwa cha dzina langa, chifukwa sadziwa wondituma Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzakuchitani zimenezi chifukwa cha dzina langa, popeza sakudziwa amene anandituma Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma izi zonse adzakucitirani cifukwa ca dzina langa, cifukwa sadziwa wondituma Ine.