John 15:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadapanda kubwera ndi kulankhula nawo, sakadakhala ndi mlandu. Koma tsopano alibe choti nkukanira mlandu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindikadadza ndi kulankhula nao sakadakhala nalo tchimo; koma tsopano alibe chowiringula pa machimo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikanapanda kubwera ndi kuyankhula nawo, sakanakhala ndi mlandu. Koma tsopano alibe choti nʼkukanira mlandu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindikadadza ndi kulankhula nao sakadakhala nalo cimo; koma tsopano alibe cowiringula pa macimo ao.