John 15:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inunso mudzandichitira umboni, popeza kuti mwakhala nane kuyambira pa chiyambi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inunso muchita umboni, pakuti muli ndi Ine kuyambira chiyambi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inunso mudzandichitira umboni Ine, popeza mwakhala nane kuchokera pachiyambi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inunso mucita umboni, pakuti muli ndi Ine kuyambira ciyambi.