John 16:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngolakwa pa za kuweruza, chifukwa Satana, mfumu ya anthu oipa a dziko lino lapansi, waweruzidwa kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
za chiweruzo, chifukwa mkulu wa dziko ili lapansi waweruzidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za chiweruzo, chifukwa wolamulira dziko lino lapansi waweruzidwa tsopano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
za ciweruziro, cifukwa mkuru wa dziko ili lapansi waweruzidwa.