John 16:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzandilemekeza, pakuti adzatenga zochokera kwa Ine nadzakudziŵitsani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iyeyo adzalemekeza Ine; chifukwa adzatenga za mwa Ine, nadzalalikira kwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzalemekeza Ine chifukwa adzatenga za Ine nadzakudziwitsani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iyeyo adzalemekeza Ine; cifukwa adzatenga za mwa Ine, nadzalalikira kwa inu.