John 16:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi nchiyani akunenachi kuti, ‘Kanthaŵi pang'ono?’ Sitikumvetsa zimene akufuna kunena.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ananena. Ichi nchiyani chimene anena, Kanthawi? Sitidziwa chimene alankhula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapitiriza kufunsana kuti, “Kodi akutanthauza chiyani, ‘kanthawi kochepa?’ Ife sitikumvetsetsa chimene Iye akuyankhula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ananena, ici nciani cimene anena, Kanthawi? Sitidziwa cimene alankhula.